Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati mpingo uli ndi gawo lalikulu kupemphelera dziko la Malawi ndi masomphenya ake. M'mawu awo pamene anakasonkhana nawo pa mwambo wa mapemphero ku mpingo wa Lingadzi CCAP mu mzinda wa Lilongwe a Chakwera anati mpingo ukuyenera kupemphelera dziko lathu ndi masomphenya a tsogolo lake, Ponena kuti aliyense akuyenera […]
The post Kumbukirani kupemphelera dziko lathu - Chakwera appeared first on Malawi 24.