Nkhondo ya masewelo a mpira wa miyendo yomwe inalipo Loweluka lathali pakati pa Silver Strikers ndi Mighty Wanderers mu mpikisano wa 2025 NBS Bank Charity Shield yakwanitsa kupanga ndalama zokwana 66.8 million Kwacha, masewelo omwe anaphopholika mu mzinda wa Lilongwe. Malinga ndi bungwe la Football Association of Malawi (FAM), mu masewelowa 61.7 million yapezeka kudzera […]
The post 2025 NBS Bank Charity Shield yaphula K66.8 million appeared first on Malawi 24.