A Polisi m’boma la Nkhotakota amanga a Frank Malaki a zaka 23 ndi mkazi wawo Enita Joseph chifukwa chofuna kugulitsa mimba pa mtengo wa K200,000. Awiriwa amafuna kugulitsa mimba ya a Joseph kwa munthu wina ochita malonda ku Nkhotakota komweko. Malingana ndi mneneri wa Polisi m’bomali a Paul Malimwe, banjali pa 7 Novembala chaka chino […]
The post Amangidwa chifukwa chofuna kugulitsa mimba ku Nkhotakota appeared first on Malawi 24.