Pomwe zotsatira za kafukufuku zasonyeza kuti anthu opitilira 15,000 ndi omwe anatenga kachirombo ka HIV chaka chatha chokha, akatswiri ati kugwiritsa ntchito njira zingapo zopewera kutenga kachiromboka, kungathandize kuchepetsa chiwerengerochi. Izi ndi malingana ndi a Ulanda Mtamba omwe ndi wa chiwiri kwa mtsogoleri wa bungwe la Civil Society Advocacy Forum omwenso ndi m’modzi mwa akatswiri […]
The post Anthu alimbikitsidwa kugwiritsa ntchito njira zingapo zopewera kutenga HIV appeared first on Malawi 24.