Anthu ochuluka mdziko muno akupitilira kukakamiza nduna yowona za mphamvu ya magetsi a Ibrahim Matola kuti abwere poyera ndikupepesa kaamba konena kuti anthu omwe akudandaula kuti Lazarus Chakwera akuyendayenda kwambiri ndi achule. Mosalingalira kuti kunena kwa ndithe ndithe nanthambwe anazitengera, a Matola anayankhula izi Lolemba pa 6 June ku Golomoti m'boma la Dedza komwe mtsogoleri […]
The post Apepese! A Malawi akwiya ponenedwa kuti achule appeared first on Malawi 24.