Timu yayikulu ya mpira wa miyendo ya Malawi 'The Flames' lero yakwapulanso Comoros ndi zigoli ziwiri kwa chete chete (2-0), mu mpikisano wa CAF African Nations Championship-CHAN pa bwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe. Zigoli za osewera wa Bullets Wongani Lungu pa mphindi ya chi 50′ ndipo patangodutsa mphindi 9 anabwera Binwell Katinji kudzasiya […]
The post Flames yamaliza kuigwira ntchito Comoros appeared first on Malawi 24.