Dziko la Malawi lalephera kulandira katemera wa Covid-19 wa AstraZeneca yemwe amayenera kufika mdziko muno lero. Watsimikiza za nkhaniyi ndi nduna ya zaumuyo a Khumbize Kandodo Chiponda omweso ndi wa pampando wa komoti yamrsogoleri wadziko yotsogolera ntchito yolimbana ndi matenda a covid-19. Malingana ndi a Kandodo Chiponda, katemerayu yemwe akugulidwa mdziko la India, walephera kufika […]
The post Katemela wa Covid-19 walephera kufika lero appeared first on Malawi 24.