Kwa nthawi yaitali nzinda wa Lilongwe wakhala ukutchedwa ‘nzinda wa fumbi’ kamba koti uli ndi misewu ya fumbi koma pano, fumbi litha kukhala mbiri yakale kamba koti boma likumanga misewu mu nzindawu. Kudzera patsamba lawo la m'chezo, a Onjezani Kenani ati tsopano nzinda wa Lilongwe ukuoneka bwino chifukwa chakumangidwa kwa misewu imeneyi ndipo iwo ati […]
The post Kenani ayamikira boma kamba kachitukuko cha nseu appeared first on Malawi 24.