Makhansala ena amu Mzinda wa Zomba komanso Phungu wamu mzindawu Bester Awali adakonza upo wofuna kuchotsa Khansala Rams Kajosolo pa udindo wa wapampando wa Komiti ya ntchito zachitukuko. Kudzela muchikalata chawo chomwe adalemba ndipo chidasayinidiwa ndi Phungu wamdera lapakati mu Mdzinda wa Zomba Bester Awali, komanso makhansala ena Christopher Jana ndi Edah Mkula ndipo chidawerengedwa […]
The post Makhansala ku Zomba akufuna kuchotsa khansala nzawo pa udindo appeared first on Malawi24.