Bwalo la Senior Resident Magistrate Joshua Nkhono ku Balaka lakana kupeleka belo kwa mayi Lilian Matako, a Zuberi Chitete komanso a Ishmael Chitete. Anthuwa akuwaganizira kuti adachita zinthu zofuna kuvulaza munthu. Powonekera ku bwalo la milandu lero masana, anthuwa akana kuvomera mulandu umene bwalo la milandu likuwazenga. Anthuwa adanjatidwa zitadziwika kuti adathandizana kupeleka chilango chomumangilira […]
The post Matako, anthu enanso awiri agonabe m'chitokosi cha Police appeared first on Malawi 24.