Mayi wa zaka 26 yemwe dzina lake ndi Omega Pemba ali m'manja mwa apolisi ku Kasungu chifukwa chotentha nyumba ya bwenzi lake ndikuwononga katundu wa ndalama zokwana K7.9 miliyoni. Mayiyu adachita izi dzana pa, 15 August, m'mudzi mwa Nkhoma kwa mfumu yayikulu Nyaza ku Kasungu Mneneri wapolisi m'boma la Kasungu a Joseph Kachikho wati Pemba […]
The post Mayi waotcha nyumba ya bwenzi lake ku Kasungu appeared first on Malawi24.