Wachiwiri kwa mtsogoleri mchipani cha Democratic Progressive (DPP) mchigawo cha pakati, a Alfred Gangata, ati mchitidwe omangana wawonjeza pomwe ati amanganso Commissioner wa apolisi chifukwa cha paint. Iwo ati commissioner wa apolisi monga wamkulu samayenera kumumanga koma amangoyenera kumuitana kuti afotokoze m'mene zinakhalira ndipo abweze ngati anatengadi zinthu. Polankhula mu program ya Times Exclusive usiku […]
The post Milandu ina ndi yongofunika kukambirana - Gangata appeared first on Malawi 24.