Akulu akulu a ndende ya Zomba atsimikiza kuti mkaidi m’modzi wa zaka 33 wathawa pomwe amagwira ntchito lero Lachiwiri. Malinga ndi m’modzi mwa akuluakulu a ndendeyi a Harrings Nyalubwe wazindikira mkaidi othawayu ngati Jimu Jabu. A Nyalubwe awuza nyumba zina zosindikiza nkhani m’dziko muno kuti Jabu wathawa m’mawa wa Lachiwiri pa 21 May 2024 pomwe […]
The post Mkaidi wathawa ku ndende ya Zomba appeared first on Malawi 24.