Zipani zotsutsa boma m’dziko muno zati mayi Annabel Mtalimanja atule pansi udindo wawo ngati mkulu wa Malawi Electoral Commission (MEC) kaamba koti alephera kugwira bwino ntchito. Zipanizi zidanena izi pa msokhano wa atolankhani omwe zipani monga Alliance For Democracy (AFORD), United Transformation Movement (UTM), Democratic Progressive Party (DPP) anachititsa ku Lilongwe. Zipanizi zinati ndizokaikitsa ngati […]
The post Mtalimanja atule pansi udindo – Zipani zotsutsa appeared first on Malawi 24.