Bungwe loyendetsa masewero a mpira wamanja mdziko muno la NAM, lati ndilokondwa ndi luso latsopano lomwe lapeza mmadera osiyanasiyana. Mlembi wamkulu wa bungweli, Yamikani Kauma wayankhula izi lero pa bwalo la zamasewero la Bingu, mumzinda wa Lilongwe komwe atsikana okwana makumi asanu ndi atatu (80), amamaliza m'bindikiro. M'bindikirowu unayamba lamulungu lapitali, pa 20 Epulo ndipo […]
The post NAM yakhutila ndi luso latsopano lomwe yapeza appeared first on Malawi 24.