Ma Kadino akulu akulu a mpingo wa katolika, omwe anapatsidwa mphamvu zosankhanso mtsogoleri wa mpingowu, agwidwa kakasi kamba kakuti sanapange chiganizo ngati nkoyenera kuti Kadino yemwe anamangidwapo kamba ka utambwali ozembetsa ndalama aloledwe kulowa mchipinda chomata kuti asankhe nawo Papa kapena ayi. Izitu zadza kamba ka Kadino Angel Becciu yemwe anali oyamba wa akulu akulu […]
The post Ndine osalakwa, ndiloleni ndisankhe nawo Papa watsopano- walira mokweza Kadino Becciu appeared first on Malawi 24.