Aphungu a Nyumba ya Malamulo lero adutsitsa bill yoti boma livomeleze ngongole ya ndalama kuchokera ku OPEC for International Development yokwana 20 million dollars yothandizira ntchito za gawo lachiwiri la Shire Valley Transformation Program (SVTP), komanso bill yolora kungongora ndalama ku European Bank zopita ku ma water board m'dziko muno. Aphunguwa ati ngongolezi ndizopindulira m'Malawi […]
The post Nyumba ya Malamulo yadutsitsa ma bill awiri okhudza ngongole appeared first on Malawi 24.