Lero pa 21 June ndi tsiku lomwe linakhazikitsidwa mwapadera padziko lonse kuti anthu azikumbukira ubwino wa nyimbo, pobweletsa pamodzi zamba zosiyanasiyana. Koma oyimba ena asonyeza kusakhutitsidwa ndi momwe tsikuli limakhalira kwathu kuno. Malawi24 inachita mwayi oyankhulana ndi ena mwa an'khala kale pa nkhani zamayimbidwe m'dziko muno kuti afotokoze m'mene tsikuli amalikumbukilira kwathu kuno. 'Ndimasangala kuti […]
The post Oyimba Ethel Kamwendo, San B ndi Collen Ali sakhutisidwa ndi World Music Day ku Malawi appeared first on Malawi 24.