…Ekhaya yasonkha nawo… Timu ya Ekhaya yomwe yangolowa kumene mu mpikisano wawukulu m'dziko muno yasonkha nawo osewela pa mndandanda wa anyamata 25 omwe mphunzitsi wa timu ya mpira wamiyendo ya Malawi Kalisto Pasuwa wayitana, kukakonzekere kuswana ndi South Africa. Malawi ikumana ndi South Africa m'masewelo oyamba a mu mpikisano wa African Nations Championship qualifiers pa […]
The post Pasuwa wayitana anyamata kukonzekera CHAN appeared first on Malawi 24.