Zatsogolo lotuluka pa belo kwa Tumpe Mtaya 'Phwedo' zidziwika mawa Lachisanu pomwe Chief Resident Magistrate Benjamin Chulu wati adzaweluza pa pempho la belo 2 koloko masana. Oyimila mbali ya boma pa mlanduwu anapempha oweluza mlandu kuti alore kuti Phwedo akhalebe omangidwa ndipo adzimusungabe kwa masiku asanu kuti amalizitse kafukufuku wawo. Koma oyimila ozengedwa anati mbali […]
The post Phwedo waonekera ku bwalo la milandu, agonabe m'chitolokosi appeared first on Malawi 24.