Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera watsimikizira bungwe la International Monetary Fund (IMF) ndi World Bank kuti dziko la Malawi lipitiliza kuika njira zabwino zokwezera chuma chake. Chakwera wanena izi pa mkumano ndi akuluakulu a ma bungwe awiriwa, Kristalina Georgieva wa IMF komanso Anna Bjerde wa Banki yaikulu pa dziko lonse mu mzinda wa […]
The post Tiyika njira zotukulira chuma cha dziko lino - Chakwera appeared first on Malawi 24.