Mkulu yemwe analembanawo nyimbo za buku lachikatolika otchedwa Pankalasiyo Pondani Phiko Phiri wamwalira m'mawa wa lero lachiwiri. A Phiri amwalira ku Nyumba kwawo ku Mua ndipo amachokera M'boma la Dedza. A Phiri ndi m'modzi mwa anthu omwe analembanawo buku la nyimbo zachikotolika ndipo imodzi mwa nyimbo zi ndi 'Chuma Chathuchi', nyimbo yomwe imayimbidwa panthawi yopereka […]
The post Yemwe anapeka nyimbo zachikatolika Pankalasiyo Phiri wamwalira appeared first on Malawi24.