Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Micheal Usi ati mzosabisa kuti ogwira ntchito ena m'boma akugwira monyentchera kotero mkoyenera kuwachotsa ntchito kuti dziko lidziyenda. Poyankhula lamulungu m'mudzi mwa a Golden m'boma la Mulanje, a Usi ati ogwira ntchito ena m'boma amangokhalira ma pepala a zinthu zofunika kuthandiza anthu amene akuvutika ku midzi pamene ena […]
The post A chidodo pantchito m'boma achotsedwe - Usi appeared first on Malawi 24.