Mtsogoleri wakale wadziko lino a Peter Mutharika akana kufunsidwa mafuso ndi bungwe lotsogolera ntchito yothana ndi katangale la Anti-Corruption Bureau (ACB) pankhani yakugwiritsidwa ntchito kwa nambala yawo ya TPIN pakugulidwa kwa simenti. A Mutharika amayenera kufunsidwa mafuso ndi akuluakulu a bungwe la ACB lero Lachiwiri pa 27 July kudzera pa intaneti potsatila kulephereka kwa nkumano […]
The post A Mutharika akana kufunsidwa mafunso ndi ACB appeared first on Malawi 24.