Abambo awiri omwe ndi a Austin Meleka komanso a Kondwani Denison amwalira atagunda sitima ya pamtunda ku Salima pamene bambo wina m'modzi wavulala kutsatira kwa ngoziyi atagona mu njanji. Malingana ndi mneneli wa apolisi ku Salima ,a Sub Inspector Rabecca Ndiwate, wati ngoziyi idachitika pakati pa usiku wapa 5 ndi 6 January, 2025 pamene iwo […]
The post Abambo awiri amwalira atagunda sitima appeared first on Malawi 24.