A nduna oona za chikhalidwe a Michael Usi amene amadziwikanso ngati Manganya ati Mulungu achita ndi a Malawi onse onyoza a Chakwera. Polankhula pa mwambo okumbukira M'busa John Chilembwe ku Chiradzulu, a Usi anadzudzula a Malawi amene ntchito yawo imakhala kudzudzula atsogoleri. Mukuona kwawo bambo Usi, amenenso ali mtsogoleri wachiwiri wa chipani cha UTM, a […]
The post Ambuye akukanthani nonse onyoza a Chakwera - watero Manganya appeared first on Malawi24.