Zoti tiri pa chisoni sizinaoneke. Zoti tate wathu ndi m'busa sizinaonekenso. Pena kumati mwina malaya ofiyira tinavala lero anamusokoneza mmaso Mo Salah kuti amayesa ndi Manchester United. Chifukwa atiswa ndipo atisambitsa chokweza. Olo naye kochi Mario Marinica wayenda wa uyo uyo pochoka pa Bingu. Zamanyazi zenizeni. Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino lero […]
The post Atipweteka, atisenda ndipo atiyalutsa: Ijipiti ya Mo Salah 4 Malawi ya Marinica 0 appeared first on Malawi24.