Timu ya Bangwe All Stars yomwe yangotuluka kumene mu ligi yayikulu ya m'dziko lino ya 2024 TNM super, tsopano yathetsedwa chifukwa cha mavuto a zachuma. Malinga ndi mwiniwake wa timu ya Bangwe, a Mphatso Jika wati malinga ndi kusowa kwa ndalama, kukhala kovuta kuti akwanitse kupitiliza kuthandiza timuyi pamene idzisewela mu masewelo a mu zigawo […]
The post Bangwe All Stars yathetsedwa appeared first on Malawi 24.