Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, asankha oweluza milandu ku bwalo lalikulu a Annabel Mtalimanja kuti atsogolere bungwe loyendetsa zisankho m'dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC). Malingana Ndi kalata imene bungwe la MEC latulutsa lero yomwe atsimikizira ndi mneneli wa bungweli a Sangwani Mwafulirwa, pogwiritsa ntchito mphamvu za lamulo la nambala 75 la […]
The post Chakwera wasankha Annabel Mtalimanja kukhala wapampando wa MEC appeared first on Malawi 24.