Bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe lakana pempho la belo la mkozi wa nyimbo Chiyanjano Mbeza yemwe anamangidwa poganizilidwa kuti wakhala akutulutsa ndi kufalitsa mauthenga onyoza mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera. Malingana ndi oweruza milandu Bernadetta Kalua yemwe amawerenga chigamulo chomwe chaperekedwa ndi oweruza milandu Roderick Michongwe, chigamulochi chapelekedwa pofuna kupeleka mpata kwa apolisi […]
The post Chiyanjano Mbeza akanizidwa kutuluka pa belo appeared first on Malawi 24.