Akuluakulu kuchokera mu komiti yoyendetsa masewero a Mpira wamiyendo mchigawo chapakati ya Central Region Football Association (CRFA), amaliza kuchita kampeni ku mazoni a m'boma la Ntcheu, yomwe cholinga chake ndikugwetsa utsogoleri omwe ulipo pano m'bomali. Msungichuma wa CRFA, Hastings Chilunga anatsogolera ma membala anayi a bungweli, Joe Twaibu, Tseka Jickson Aluya komaso Paul Kampira pa […]
The post CRFA yamaliza kampeni ku Ntcheu appeared first on Malawi 24.