Fikitsani uthengawu ku Mangochi kwa a Mutharika: zobwelera m'boma ndi maloto chabe, a Malawi onse maso nga! pa Chakwera, watero ndi nduna ya Maboma Aang'ono a Richard Chimwendo Banda. Polankhula potsekera zokambirana mu nyumba ya malamulo lero, a Chimwendo Banda ati chipani chotsutsa cha DPP chinatuluka m'boma ndipo sichibweleranso. Iwo ati a Malawi ambiri akukumbukirabe […]
The post DPP sidzabweleranso m'boma ndipo 2025 Chakwera awina ndi 70% - Chimwendo appeared first on Malawi 24.