Nthambi yowona za nyengo yati pali kuthekera koti namondwe yemwe akuyembekezeka kubadwa mnyanja ya m'chere ya India, akhoza kudzafika kapena kuyandikira kum'mwera kwa dziko lino. Malinga ndi nthambiyi, Namondweyu sanabadwe koma akuyembekezeka kubadwa mu Nyanja ya Mchere ya India pakati pa mayiko a Madagascar ndi Mozambique pofika Lamulungu lino pa 10 March, 2024. 'Pali chiyembekezo […]
The post Dziko lino lili pa chiopsezo cholandiraso namondwe appeared first on Malawi 24.