Fostina Mbemba ndi amene wathamanga kuposa atsikana anzake mu mpikisano wa Mzuzu City Half Marathon lero. Mtsikanayu analibutsa liwiro ngati kulibe mawa ndipo iye anathamanga mtunda okwana 21 kilomitazi pa ola limodzi ndi mphindi zokwana makumi awili ndi zisanu. Wachiwiri kupambana ndi Teleza Master ndipo iye anathamanga makilomita okwana 21 mu ola limodzi ndi mphindi […]
The post Fostina Mbemba wapambana mpikisano wa Mzuzu Half Marathon appeared first on Malawi 24.