Mtsikana wazaka khumi wafa atalumidwa ndi galu pa malo ena omwetsera mafuta agalimoto mu mzinda wa Lilongwe. Malingana ndi lipoti la apolisi lomwe tsamba lino lawona, mtsikanayu wazindikilidwa ngati Ellen Chawanda yemwe wakumana ndi tsokali lachiwiri pa 25 July, 2023. Lipotili likusonyeza kuti patsikuli Ellen anali ndi mkulu wake Nellie Chaola omwe anali akuchokera mbali […]
The post Galu wa pothilira mafuta wapha mtsikana wa zaka 10 appeared first on Malawi24.