Oyimba Gibo Pearson wapulumuka pa ngozi ya pansewu pomwe galimoto yomwe amayendetsa inasadabuzika Lolemba ku Blantyre. Woyimbayu amachoka kokaimba ku Zomba. Malingana ndi uthenga omwe tawona ochokera kwa woyimbayu yemwe amadziwika ndi nyimbo za lokolo, ngoziyi yachitika pa malo ena otchedwa Mapanga mu nsewu wa Blantyre-Zomba. Woyimba wa ku Phalombe-yu wati atafika pa malowa paulendo […]
The post Gibo Pearson wapulumuka pangozi ya galimoto appeared first on Malawi 24.