Ngati mumakhala mukufunafuna mwayi wa nyumba ku Area 43 anaimba Tay Grin kuja ndiye sunthirani pafupi. Ndi kutheka mayankho anu muwapeza pano. A bwalo ati nyumba ya a Paul Mphwiyo ilandidwe ndithu. Oweruza milandu wa ku bwalo lalikulu Mayi Ruth Chinangwa akana kuchitira chisoni mkazi wa Paul Mphwiyo amene amafuna kuti bwalo liyimitse kaye kuwalanda […]
The post Gulitsani zimenezi - a bwalo agangalama, ati nyumba ya Mphwiyo ipitebe pa msika basi appeared first on Malawi 24.