…watsindika zakufunika kwa ulamuliro wa mzigawo Mtsogoleri wa chipani cha Alliance for Democracy (AFORD) Enoch Chihana wati chipani chawo sichilowaso mu mgwirizano ndi zipani zina pa chisankho chikubwerachi ponena kuti akuona kuti nthawi yoti AFORD ilowe m’boma yakwana. A Chihana anayankhula izi Lolemba pa msonkhano omwe chipanichi chinachititsa ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre komweso […]
The post Ino ndi nthawi yathu, sitikhalaso m'nkhwapa mwa chipani china, watero Chihana appeared first on Malawi24.