…waitanitsa ma demo sabata yamawa… M’modzi mwa anthu odziwika bwino pa ndale omweso ndi membala wa chipani cha UTM, a Bon Kalindo, adzudzula atsogoleri a boma kaamba kolephera kuyendetsa bwino dziko lino. A Kalindo omwe amadziwikaso ndi dzina la Winiko amayankhula izi pomwe amacheza ndi wailesi ya kanema ya Rainbow Lachinayi ndipo anati ndiokhumudwa kwambiri […]
The post Kalindo wasambwadza boma appeared first on Malawi 24.