Ena mwa ogwira ntchito m'boma ku Kasungu anauza Phungu wawo Ken Kandodo kuti akameme aphungu amzake kuti boma liwakwezere malipiro. Poyankhula pa mkumano omwe a Kandodo anachititsa ndi anthuwo, m'modzi mwa anthu ogwira ntchito m'boma anati; 'Pitani ndithu mukawanong'oneze kuti malipo aonjezere ndi 44%, paja olira samutseka pakamwa, komanso sachita kumupangira. Pajatu tilipo 300,000 ndipo […]
The post Kauzeni aphungu amzanu 44% itheke - Ogwira ntchito m'boma auza Kandodo appeared first on Malawi 24.