Bugwe la Copyright Society of Malawi (COSOMA), kudzera mwa wapampando wa bungweli a Chimwemwe Mhango, ati Lucius Banda sanagugepo chiyambileni kuyimba kwake zaka zoposa 30 zapitazo, zomwe zukuwonetseratu mphamvu zomwe Mulungu anamupatsa pa kapekedwe komanso kayimbidwe kake ka nyimbo ku Malawi. Mu ma uthenga a kulira kwawo pa mwambo wa maliro a katswiri wa zimbale […]
The post Lucius Banda Sanagugepo appeared first on Malawi 24.