Bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lero latseka malo omwetsera mafuta a Ntcheu Puma Fueling Station chifukwa chophwanya malamulo a za mphamvu, pogulitsa mafuta mu zigubu ndi mu ma drum kwa mavenda. M'modzi mwa akuluakulu a bungwe la MERA, a Vitumbiko Sakala atsimikiza za nkhaniyi ponena kuti bungwe la MERA lidatulutsa kalata kuletsa kugulitsa […]
The post MERA yatseka malo omwetsera mafuta a Ntcheu Puma appeared first on Malawi 24.