Tsoka likalimba amakulumadi ndi galu wako yemwe, ku m'mawa-ku adzukulu am'mudzi wa Maula, m'boma la Mchinji, T/A Ndawambe, amangilira kumtengo mfumu yawo a Juma kaamba koti asokoneza ndalama zachipepeso zomwe zimayenera kupita kwa anamfedwa. Malingana ndi yemwe watiuza nkhaniyi ndipo ali kumwamboko, pali chikhulupiliro kuti mfumu Juma ndalamazi yasewelera njuga ya mtundu wa Aviator yomwe […]
The post Mfumu imangiliridwa ku mtengo appeared first on Malawi 24.