Chimodzi mwazipani zikuluzikulu mumgwirizano wa Tonse, UTM, chauza anthu mdziko muno kuti asiye kuyambitsa nkhani zomwe zitha kudanitsa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ndi wachiwiri wawo a Saulos Chilima. Nkhaniyi ikutsatira chithunzi chomwe chikuyenda pa masamba amchezo chomwe pali nkhope ya wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino Saulos Chilima ndipo palembedwa kuti momwe a […]
The post Musawadanitse a Chakwera ndi a Chilima - UTM appeared first on Malawi 24.