…ati anthu akudzipha kwambiri kaamba koti alibe chiyembekezo…ati MCP ikufuna kudzabela chisankho 2025 Mtsogoleri wakale wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Peter Mutharika, asambwadza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ponena kuti mavuto onse omwe ali mdziko muno ndi kaamba koti a Chakwera alephera kulamulira. A Mutharika […]