Mtsogoleri wa zipani zotsutsa kunyumba ya malamulo a Kondwani Nankhumwa wati kuyambira 2025, iye ndi amene akhale akutsogolera dziko la Malawi. Polankhula ndi a Brian Banda, a Nankhumwa ati iwo atenga chipani cha DPP kuchokera kwa a Peter Mutharika. 'Konveshoni ya chaka chino ya DPP, ine ndikawina ndipo ndikatenga u President wa chipani chimenechi,' anatero […]
The post Ndikawina konveshoni ya DPP ndipo ndizakhala mtsogoleri wa Malawi — Nankhumwa appeared first on Malawi24.