Amene akutsogolera zionetsero zosagwirizana ndi kukwera kwa mitengo ya zinthu Bon 'Winiko' Kalindo wanenetsa kuti akufuna akumane ndi mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera. Kalindo amene adalepherana kumvana ndi nduna zaboma pamkumano omwe anali nawo sabata lapitali, wati ndiokonzeka kukumana ndi mtsogoleri wa dziko lino kuti akambirane m’mene angasinthire zinthu. Polankhula ndi nyumba zoulusa nkhani, […]
The post Ndikufuna kukumana ndi Chakwera – watero Winiko appeared first on Malawi 24.