Mipando ya kunyumba ya malamulo ayiveka nsalu yatsopano. Poyamba nyumbayi idali ndi mipando ya blue ndipo pano aikutira nsalu ina yomwe ndi mbendera ya dziko lino. Mipando mnyumbayi, ndiyomwe ija yakale koma yangokutilidwa nsalu ina ndipo mbali ina ya mpandowo ikuonekabe blue. Pa 17 November 2023 Ishmael Onani, phungu wa dera la ku m'mwera m'boma […]
The post Nyumba ya Malamulo isintha nsalu ya mipando appeared first on Malawi 24.