Gulu la anthu ogwira ntchito zaumoyo omwe sanalembedwebe ntchito, awopseza kuti apitilira ndi ganizo lawo lokasumira unduna wa zaumoyo pa zotsamwitsa zomwe zinachitika pa ndondomeko yolemba anthu ntchito ngati undunawu suwalemba ntchito nsanga. Nkhaniyi inayamba mu February chaka chino pomwe unduna wa zaumoyo unatulutsa maina a ogwira ntchito zaumoyo omwe boma linawalemba ntchito m'magulu osiyanasiyana. […]
The post Ogwira ntchito zaumoyo awopsyezanso kutengera unduna ku khothi appeared first on Malawi 24.