Ophunzira wina wa zaka khumi (10) m'boma la Phalombe, wafa atagundidwa ndi njinga yamoto dzulo Lamulungu pomwe oyendetsa njingayi anakanika kuyiwongolera kamba kothamanga kwambiri. M'neneri wa polisi ya Phalombe, a Jimmy Kapanja, watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti ophunzirayu yemwe dzina lake Chrispin Makalani, yemwe anali kuphunzira pa sukulu ya pulayimale ya Namikango. Malingana ndi m'neneliyu, […]
The post Ophunzira wafa atagundidwa ndi njinga yamoto appeared first on Malawi 24.